Psalms 89:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwalimbikitsa amaliwongo ake, mwakondwetsa adani ake onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munakweza dzanja lamanja la iwo omsautsa; munakondweretsa adani ake onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwakweza dzanja lamanja la adani ake; mwachititsa kuti adani ake akondwere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munakweza dzanja lamanja la iwo omsautsa; Munakondweretsa adani ace onse.