Psalms 89:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inde, mwabunthitsa lupanga lake, ndipo simudamlimbitse pa nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munapinditsa kukamwa kwake kwa lupanga lake, osamuimika kunkhondo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwabunthitsa lupanga lake, simunamuthandize pa nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munapinditsa kukamwa kwace kwa lupanga lace, Osamuimika kunkhondo.