Psalms 89:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwamchotsera ndodo yachifumu m'manja, ndipo mwataya pansi mpando wake wachifumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munaleketsa kuwala kwake, ndipo munagwetsa pansi mpando wachifumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwathetsa kukongola kwa ulemerero wake ndipo mwagwetsa pansi mpando wake waufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munaleketsa kuwala kwace, Ndipo munagwetsa pansi mpando wacifumu wace.