Psalms 89:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwamkalambitsa msanga, mwamkuta ndi manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munafupikitsa masiku a mnyamata wake; munamkuta nao manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwachepetsa masiku a unyamata wake; mwamuphimba ndi chofunda chochititsa manyazi. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munafupikitsa masiku a mnyamata wace; Munamkuta nao manyazi.