Psalms 89:46 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mpaka liti, Inu Chauta? Kodi mudzandibisalira mpaka muyaya?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzabisala kosatha kufikira liti, Yehova; ndi kuzaza kwanu kudzatentha ngati moto kufikira liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mpaka liti Yehova? Kodi mudzadzibisa mpaka kalekale? Mpaka liti ukali wanu udzayaka ngati moto?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzabisala kosatha kufikira liti, Yehova; Ndi kuzaza kwanu kudzatentha ngati moto kufikira liti?