Psalms 89:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbukirani kuti masiku a moyo wanga ndi ochepa. Zoonadi, mudalenga anthu onse kuti akhale a moyo waufupi kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani kuti nthawi yanga njapafupi; munalengeranji ana onse a anthu kwachabe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani kuti masiku a moyo wanga ndi ochepa pakuti munalenga kwachabe anthu onse!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukilani kuti nthawi yanga njapafupi; Munalengeranji ana onse a anthu kwacabe?