Psalms 89:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zakumwamba zimatamanda zodabwitsa zanu, Inu Chauta, zimatamanda kukhulupirika kwanu mu msonkhano wa oyera mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kumwamba kudzalemekeza zodabwitsa zanu, Yehova; chikhulupiriko chanunso mu msonkhano wa oyera mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayiko akumwamba amatamanda zozizwitsa zanu Yehova, kukhulupirika kwanunso, mu msonkhano wa oyera mtima anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kumwamba kudzalemekeza zodabwiza zanu, Yehova; Cikhulupiriko canunso mu msonkhano wa oyera mtima.