Psalms 89:50 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye, kumbukirani kunyozedwa kwa mtumiki wanune, ndakhala ndikupirira chamumtima chipongwe cha anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani, Ambuye, chotonzera atumiki anu; ndichisenza m'chifuwa mwanga chochokera kumitundu yonse yaikulu ya anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani, Ambuye momwe mtumiki wanu wanyozedwera, momwe ndakhalira ndi kusunga mu mtima mwanga mawu a pangano a anthu a mitundu yonse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukilani, Ambuye, cotonzera atumiki anu; Ndicisenza m'cifuwa mwanga cacokera ku mitundu yonse yaikuru ya anthu;