Psalms 89:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbukirani kuti amene akundinyozawo ndi adani anu, Inu Chauta, iwo akunyoza Wodzozedwa wanu paliponse pamene waponda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chimene adani anu, Yehova, atonza nacho; chimene atonzera nacho mayendedwe a wodzozedwa wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mawu achipongwe amene adani anu akhala akunyoza, Inu Yehova, ndi mawu amene akhala akunyoza mayendedwe onse a wodzozedwa wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cimene adani anu, Yehova, atonza naco; Cimene atonzera naco mayendedwe a wodzozedwa wanu.