Psalms 89:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu ndiye amene amamuwopa mu msonkhano wa anthu oyera mtima, ndiye wamkulu ndi wolemekezeka pakati pa onse omzungulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiye Mulungu, ayenera kumuopa kwambiri m'upo wa oyera mtima, ndiye wochititsa mantha koposa onse akumzinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mu msonkhano wa oyera mtima Mulungu amaopedwa kwambiri; Iye ndiye wochititsa mantha kupambana onse amene amuzungulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiye Mulungu, ayenera kumuopa kwambiri m'upo wa oyera mtima, Ndiye wocititsa mantha koposa onse akumzinga.