Psalms 89:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumalamulira nyanja yaukali. Mafunde ake akakwera, Inu mumaŵakhalitsa bata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu ndinu wakuchita ufumu pa kudzikuza kwa nyanja; pakuuka mafunde ake muwachititsa bata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumalamula nyanja ya mafunde awukali; pamene mafunde ake awundana Inu mumawakhalitsa bata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu ndinu wakucita ufumu pa kudzikuza kwa nyanja; Pakuuka mafunde ace muwacititsa bata.