Psalms 9:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amadziŵa dzina lanu, Inu Chauta, amakukhulupirirani, pakuti Inu Chauta simuŵasiya anthu okufunitsitsani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo iwo akudziwa dzina lanu adzakhulupirira Inu; pakuti, Inu Yehova, simunawasiya iwo akufuna Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene amadziwa dzina lanu adzadalira Inu, pakuti Inu Yehova, simunawatayepo amene amafunafuna inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo akudziwa dzina lanu adzakhulupirira Inu; Pakuti, Inu Yehova, simunawasiya iwo akufuna Inu.