Psalms 9:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imbani nyimbo zotamanda Chauta amene amakhala ku Ziyoni. Lalikani za ntchito zake kwa anthu a mitundu yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Imbirani zoyamika Yehova, wokhala ku Ziyoni; lalikirani mwa anthu ntchito zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imbani nyimbo zamatamando kwa Yehova, ali pa mpando waufumu mu Ziyoni; lengezani pakati pa mitundu ya anthu zimene wachita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yimbirani zoyamika Yehova, wokhala ku Ziyoni; Lalikirani mwa anthu nchito zace.