Psalms 9:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Iye amachitira chifundo anthu ozunzika, salephera kumva kulira kwao ndipo amalanga anthu oŵazunzawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Iye wofuna chamwazi awakumbukira; saiwala kulira kwa ozunzika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Iye amene amabwezera chilango akupha anzawo wakumbukira; Iye salekerera kulira kwa ozunzika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Iye wofuna camwazi awakumbukila; Saiwala kulira kwa ozunzika.