Psalms 9:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundikomere mtima, Inu Chauta. Onani m'mene akundisautsira anthu ondida. Inu mumandipulumutsa ku imfa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndichitireni chifundo, Yehova; penyani kuzunzika kwanga kumene andichitira ondidawo, inu wondinyamula kundichotsa kuzipata za imfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, onani momwe adani anga akundizunzira! Chitireni chifundo ndipo ndichotseni pa zipata za imfa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndicitireni cifundo, Yehova; Penyani kuzunzika kwanga kumene andicitira ondidawo, Inu wondinyamula kundicotsa ku zipata za imfa;