Psalms 9:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti ndithe kuyamika ntchito zanu zonse, pakati pa anthu anu a mu Ziyoni. Zoonadi ndidzakondwa chifukwa mwandipulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti ndibukitse lemekezo lanu lonse; pa bwalo la mwana wamkazi wa Ziyoni, ndidzakondwera nacho chipulumutso chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti ndilengeze za matamando anu pa zipata za ana aakazi a Ziyoni, kuti pamenepo ndikondwere ndi chipulumutso chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ndibukitse lemekezo lanu lonse; Pa bwalo la mwana wamkazi wa Ziyoni, Ndidzakondwera naco cipulumutso canu.