Psalms 9:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akunja agwera m'mbuna yokumba iwo omwe. Phazi lao lakodwa mu ukonde wobisika wotcha iwo omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amitundu anagwa m'mbuna imene anaikumba, lakodwa phazi lao muukonde anautcha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitundu ya anthu yagwa mʼdzenje limene yakumba; mapazi awo akodwa mu ukonde umene anawubisa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amitundu anagwa m'mbuna imene anaikumba: Lakodwa phazi lao muukonde anaucha.