Psalms 9:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta wadziwulula yekha, pakuweruza molungama, koma anthu oipa akodwa mu msampha wotcha iwo omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anadziwika Yehova, anachita kuweruza, woipayo anakodwa ndi ntchito ya manja ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amadziwika ndi chilungamo chake; oyipa akodwa ndi ntchito za manja awo. Higayoni. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anadziwika Yehova, anacita kuweruza: Woipayo anakodwa ndi nchito ya manja ace.