Psalms 9:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anthu oipa adzapita ku dziko la anthu akufa, ndiye kuti anthu onse amene amakana Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oipawo adzabwerera kumanda, inde amitundu onse akuiwala Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Oyipa amabwerera ku manda, mitundu yonse imene imayiwala Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oipawo adzabwerera kumanda, Inde amitundu onse akuiwala Mulungu.