Psalms 9:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakondwa ndi kusangalala chifukwa cha Inu, ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu, Inu Wopambanazonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakondwerera ndi kusekera mwa Inu; ndidzaimbira dzina lanu, Wam'mwambamwamba Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakondwa ndi kusangalala mwa inu; Ndidzayimba nyimbo zamatamando pa dzina lanu, Inu Wammwambamwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakondwerera ndi kusekera mwa Inu; Ndidzayimbira dzina lanu, Wam'mwambamwamba Inu.