Psalms 9:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, aopseni anthuwo. Akunjawo adziŵe kuti iwo ndi anthu chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muwachititse mantha, Yehova; adziwe amitundu kuti ali anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akantheni ndi mantha aakulu, Inu Yehova; mitundu idziwe kuti iwo ndi anthu wamba. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muwacititse mantha, Yehova; Adziwe amitundu kuti ali anthu.