Psalms 9:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukangofika, adani anga amathaŵa, amaphunthwa ndi kufa pamaso panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pobwerera m'mbuyo adani anga, akhumudwa naonongeka pankhope panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani anga amathawa, iwo amapunthwa ndi kuwonongedwa pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pobwerera m'mbuyo adani anga, Akhumudwa naonongeka pankhope panu,