Psalms 9:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwaimba mlandu mafuko a anthu, mwaononga anthu oipa. Adzaiŵalika mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwadzudzula amitundu, mwaononga woipayo, mwafafaniza dzina lao kunthawi yonka muyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwadzudzula mitundu ya anthu ndipo mwawononga anthu oyipa; Inu mwafafaniza dzina lawo kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwadzudzula amitundu, mwaononga woipayo, Mwafafaniza dzina lao ku nthawi Yomka muyaya.