Psalms 9:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta amakhala pa mpando wake waufumu nthaŵi zonse, adakhazika mpando wake kuti aziweruza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehova akhala chikhalire, anakonzeratu mpando wachifumu wake kuti aweruze.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akulamulira kwamuyaya; wakhazikitsa mpando wake waufumu woweruzira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehova akhala cikhalire: Anakonzeratu mpando wacifumu wace kuti aweruze.