Psalms 90:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndani amadziŵa kukula kwa mkwiyo wanu ndi ukali wanu, kupambana anthu okuwopani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adziwa mphamvu ya mkwiyo wanu ndani, ndi ukali wanu monga ayenera kukuopani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndani amadziwa mphamvu ya mkwiyo wanu? Pakuti ukali wanu ndi waukulu ngati ulemu umene uyenera Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adziwa mphamvu ya mkwiyo wanu ndani, Ndi ukali wanu monga ayenera kukuopani?