Psalms 90:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tisangalatseni masiku ambiri monga masiku amene mudatisautsira, zaka zambiri monga zaka zimene tidaona mavuto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tikondweretseni monga mwa masiku mudatizunzawa, ndi zaka tidaona choipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tisangalatseni masiku ambiri monga masiku amene mwatisautsa, kwa zaka zambiri monga momwe tinaonera mavuto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tikondweretseni monga mwa masiku mudatizunzawa, Ndi zaka tidaona coipa.