Psalms 90:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulole kuti ntchito zanu ziwoneke kwa atumiki anu, mphamvu zanu zaulemerero ziwoneke kwa ana ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chochita Inu chioneke kwa atumiki anu, ndi ulemerero wanu pa ana ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ntchito zanu zionetsedwe kwa atumiki anu, kukongola kwanu kwa ana awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cocita Inu cioneke kwa atumiki anu, Ndi ulemerero wanu pa ana ao.