Psalms 90:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mapiri asanabadwe, ndipo musanalenge dziko lapansi ndi pokhala anthu, ndinu Mulungu kuyambira muyaya mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asanabadwe mapiri, kapena musanalenge dziko lapansi, ndi lokhalamo anthu, inde, kuyambira nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha, Inu ndinu Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mapiri asanabadwe, musanalenge nʼkomwe dziko lapansi ndi dziko lonse, kuyambira muyaya mpaka muyaya Inu ndinu Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asanabadwe mapiri, Kapena musanalenge dziko lapansi, ndi lokhalamo anthu, Inde, kuyambira nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha, Inu ndinu Mulungu.