Psalms 90:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti zaka chikwi chimodzi pamaso panu zili ngati dzulo chabe, kapena ngati kamphindi chabe kausiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti pamaso panu zaka zikwi zikhala ngati dzulo, litapita, ndi monga ulonda wa usiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti zaka 1,000 pamaso panu zili ngati tsiku limene lapita kapena ngati kamphindi ka usiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti pamaso panu zaka zikwi Zikhala ngati dzulo, litapita, Ndi monga ulonda wa usiku.