Psalms 90:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumachotsa moyo wa anthu mwadzidzidzi. Ali ngati maloto, ali ngati udzu wongotsitsimuka m'maŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muwatenga ngati ndi madzi aakulu, akhala ngati tulo; mamawa akhala ngati msipu wophuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mumasesa anthu mʼtulo ta imfa, iwo ali ngati udzu watsopano wa mmawa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muwatenga ngati ndi madzi akulu, akhala ngati tulo; Mamawa akhala ngati msipu waphuka.