Psalms 90:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu masiku athu amachepa chifukwa cha mkwiyo wanu, zaka zathu zimatha ngati kuusa moyo chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti masiku athu onse apitirira m'ukali wanu; titsiriza moyo wathu ngati lingaliro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Masiku athu onse amatha ali pansi pa ukali wanu; timatsiriza zaka zathu ndi kubuwula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti masiku athu onse apitirira m'ukali wanu; Titsiriza moyo wathu ngati lingaliro.