Psalms 91:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu amene amakhala m'linga la Wopambanazonse, iye amene amakhala mumthunzi mwa Mphambe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye amene akhala pansi m'ngaka yake ya Wam'mwambamwamba adzagonera mu mthunzi wa Wamphamvuyonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amene amakhala mu mthunzi wa Wammwambamwamba adzapuma mu mthunzi wa Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye amene akhala pansi m'ngaka yace ya Wam'mwambamwamba Adzagonera mu mthunzi wa Wamphamvuyonse.