Psalms 91:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzakunyamula m'manja mwao, kuwopa kuti phazi lako lingapweteke ndi mwala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzakunyamula pa manja ao, ungagunde phazi lako pamwala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo adzakunyamula ndi manja awo, kuti phazi lako lisagunde pa mwala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzakunyamula pa manja ao, Ungagunde phazi lako pamwala.