Psalms 91:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sudzaopanso mliri wogwa usiku, kapena zoononga moyo masana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena mliri woyenda mumdima, kapena chionongeko chakuthera usana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapena mliri umene umayenda mu mdima, kapena zowononga za pa nthawi ya masana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena mliri woyenda mumdima, Kapena cionongeko cakuthera usana.