Psalms 91:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anzako chikwi chimodzi angathe kuphedwa pambali pakopa, kapena zikwi khumi ku dzanja lako lamanja, koma iwe zoopsazo sizidzakukhudza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pambali pako padzagwa chikwi, ndi zikwi khumi pa dzanja lamanja lako; sichidzakuyandikiza iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu 1,000 atha kufa pambali pako, anthu 10,000 kudzanja lako lamanja, koma zoopsazo sizidzafika pafupi ndi iwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pambali pako padzagwa cikwi, Ndi zikwi khumi pa dzanja lamanja lako; Sicidzakuyandikiza iwe.