Psalms 91:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uzingopenya ndi maso ako, ndipo udzaona m'mene amalangidwira anthu ochita zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma udzapenya ndi maso ako, nudzaona kubwezera chilango oipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Udzapenya ndi maso ako ndipo udzaona mmene anthu oyipa amalangidwira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma udzapenya ndi maso ako, Nudzaona kubwezera cilango oipa.