Psalms 92:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkwabwino kuthokoza Chauta, kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, Inu Wopambanazonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo, Nyimbo ya pa Sabata. Nkokoma kuyamika Yehova, ndi kuimbira nyimbo dzina lanu, Wam'mwambamwamba Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo. Nyimbo ya pa tsiku la Sabata. Nʼkwabwino kutamanda Yehova ndi kuyimbira nyimbo dzina lanu, Inu Wammwambamwamba,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nkokoma kuyamika Yehova, Ndi kuyimbira nyimbo dzina lanu, Wam'mwambamwamba Inu: