Psalms 92:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine mwandilimbitsa ngati njati. Mwandidzoza ndi mafuta atsopano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma munakweza nyanga yanga ngati ya njati; anandidzoza mafuta atsopano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwakweza nyanga yanga ngati nyanga ya njati; mafuta abwino akhuthulidwa pamutu wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munakweza nyanga yanga ngati ya njati; Anandidzoza mafuta atsopano.