Psalms 92:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maso anga aona kuwonongeka kwa adani anga, makutu anga amva za kugwa kwa adani ondiwukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Diso langa lapenya chokhumba ine pa iwo ondilalira, m'makutu mwanga ndamva chokhumba ine pa iwo akuchita zoipa akundiukira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maso anga aona kugonjetsedwa kwa olimbana nane, makutu anga amva za kugwa kwa amaliwongo anga oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Diso langa lapenya cokhumba ine pa iwo ondilalira, M'makutu mwanga ndamva cokhumba ine pa iwo akucita zoipa akundiukira.