Psalms 92:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu okondweretsa Mulungu zinthu zimaŵayendera bwino ngati mitengo ya mgwalangwa, amakula ngati mikungudza ya ku Lebanoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolungama adzaphuka ngati mgwalangwa; adzakula ngati mkungudza wa ku Lebanoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu olungama adzaphuka ngati mtengo wa mgwalangwa, adzakula ngati mkungudza wa ku Lebanoni;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolungama adzaphuka ngati mgwalangwa; Adzakula ngati mkungudza wa ku Lebano.