Psalms 92:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ali ngati mitengo yookedwa m'Nyumba ya Chauta, yokondwa m'mabwalo a Nyumba ya Mulungu wathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ookedwa m'nyumba ya Yehova, adzaphuka m'mabwalo a Mulungu wathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
odzalidwa mʼnyumba ya Yehova, adzakula bwino mʼmabwalo a Mulungu wathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ookedwa m'nyumba ya Yehova, Adzaphuka m'mabwalo a Mulungu wathu.