Psalms 92:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
poimba nyimbo zokoma ndi gitara, zeze ndi pangwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa choimbira cha zingwe khumi ndi pachisakasa; pazeze ndi kulira kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuyimbira nyimbo choyimbira cha zingwe khumi ndi mayimbidwe abwino a zeze.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa coyimbira ca zingwe khumi ndi pacisakasa; Pazeze ndi kulira kwace.