Psalms 92:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, mwandisangalatsa ndi ntchito zanu. Motero ndikufuula ndi chimwemwe chifukwa cha zimene Inu mwachita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza Inu, Yehova, munandikondweretsa ndi kuchita kwanu, ndidzafuula mokondwera pa ntchito ya manja anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Inu mumandisangalatsa ndi ntchito zanu, Inu Yehova; Ine ndikuyimba mwachimwemwe pa ntchito ya manja anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza Inu, Yehova, munandikondweretsa ndi kucita kwanu, Ndidzapfuula mokondwera pa nchito ya manja anu.