Psalms 92:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngakhale anthu oipa aziphuka ngati udzu, ndipo anthu ochimwa zinthu ziziŵayendera bwino, kwao nkuwonongeka kwamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chakuti pophuka oipa ngati msipu, ndi popindula ochita zopanda pake; chitero kuti adzaonongeke kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti ngakhale anthu oyipa aphuka ngati udzu ndipo anthu onse ochita zoyipa apindula, adzawonongedwa kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cakuti pophuka oipa ngati msipu, Ndi popindula ocita zopanda pace; Citero kuti adzaonongeke kosatha: