Psalms 92:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu nokha Chauta, ndinu Wopambanazonse mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Inu, Yehova, muli m'mwamba kunthawi yonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Yehova, ndinu wokwezedwa kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Inu, Yehova, muli m'mwamba ku nthawi yonse.