Psalms 93:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndiye mfumu. Wavala ulemerero, wavala mphamvu ngati lamba. Iye adakhazikitsa dziko lapansi, silidzagwedezeka konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova achita ufumu; wadziveka ndi ukulu; wadziveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'chuuno; dziko lomwe lokhalamo anthu likhakizika, silidzagwedezeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akulamulira, wavala ulemerero; Yehova wavala ulemerero ndipo wadzimangirira mphamvu, dziko lonse lakhazikika kolimba; silingasunthidwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova acita ufumu; wadzibveka ndi ukulu; Wadzibveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'cuuno; Dziko lomwe lokhalamo anthu likhazikika, silidzagwedezeka.