Psalms 93:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mpando wanu waufumu, Inu Chauta, mudaukhazikitsa kuyambira makedzana, Inu ndinu amuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mpando wachifumu wanu ukhazikika kuyambira kale lija; Inu ndinu wosayambira ndi kale lomwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpando wanu waufumu unakhazikika kalekale; Inu ndinu wamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mpando wacifumu wanu ukhazikika kuyambira kale lija; Inu ndinu wosayambira ndi kale, lomwe.