Psalms 93:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amene ali pamwamba, ndi wamphamvu kupambana kulindima kwa madzi ambiri, ndi wamphamvu kuposa mafunde am'nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova Wam'mwamba ndiye wamphamvu, wakuposa mkokomo wa madzi ambiri, ndi mafunde olimba a nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndi wamphamvu kupambana mkokomo wa madzi ambiri, ndi wamphamvu kupambana mafunde a nyanja, Yehova mmwamba ndi wamphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova Wam'mwamba ndiye wamphamvu, Wakuposa mkokomo wa madzi ambiri, Ndi mafunde olimba a nyanja.