Psalms 94:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amadziŵa maganizo a anthu kuti ndi mpweya chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova adziwa zolingalira za munthu, kuti zili zachabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amadziwa maganizo a munthu; Iye amadziwa kuti maganizowo ndi achabechabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova adziwa zolingalira za munthu, Kuti ziri zacabe.