Psalms 94:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, ngwodala munthu amene mumamlangiza, amene mumamphunzitsa ndi malamulo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala munthu amene mumlanga, Yehova; ndi kumphunzitsa m'chilamulo chanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wodala munthu amene Inu Yehova mumamulangiza, munthu amene mumamuphunzitsa kuchokera mulamulo lanu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala munthu amene mumlanga, Yehova; Ndi kumphunzitsa m'cilamulo canu;